2 Mafumu 10:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehu anasonkhanitsa anthu onse pamodzi, nanena nao, Ahabu anatumikira Baala pang'ono, koma Yehu adzamtumikira kwambiri.

2 Mafumu 10

2 Mafumu 10:8-19