2 Akorinto 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsopano ndikondwera, sikuti mwangomvedwa cisoni, koma kuti mwamvetsedwa cisoni ku kutembenuka mtima; pakuti munamvetsedwa cisoni ca kwa Mulungu, kuti tisakusowetseni m'kanthu kali konse.

2 Akorinto 7

2 Akorinto 7:1-16