2 Akorinto 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuti ngakhale ndakumvetsani cisoni ndi kalata uja, sindiwawapo mtima, ndingakhale ndinawawa mtima; pakuti ndiona kuti kalata uja anakumvetsani cisoni, ngakhale kwa nthawi yokha.

2 Akorinto 7

2 Akorinto 7:3-13