2 Akorinto 5:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tiri atumiki m'malo mwa Kristu, monga ngati Mulungu alikudandaulira mwa ife; tiumiriza inu m'malo mwa Kristu, yanjanitsidwani ndi Mulungu,

2 Akorinto 5

2 Akorinto 5:10-21