2 Akorinto 5:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiko kunena kuti Mulungu anali mwa Kristu, alinkuyanjanitsa dziko lapansi kwa Iyeyekha, osawawerengera zolakwa zao; ndipo anaikiza kwa ife mau a ciyanjanitso,

2 Akorinto 5

2 Akorinto 5:11-21