2 Akorinto 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti sitikhala monga ambiriwo, akucita malonda nao mau a Mulungu; koma monga mwa coona mtima, koma monga mwa Mulungu pamaso pa Mulungu, tilankhula mwa Kristu.

2 Akorinto 2

2 Akorinto 2:7-17