2 Akorinto 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ngati ndikafuna kudzitamandira, sindidzakhala wopanda nzeru; pakuti ndidzanena coonadi; koma ndileka, kuti wina angandiwerengere ine koposa kumene andiona ine, kapena amva za ine.

2 Akorinto 12

2 Akorinto 12:1-10