1 Yohane 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Umo cidaoneka cikondi ca Mulungu mwa ife, kuti Mulungu anamtuma Mwana wace wobadwa yekha alowe m'dziko lapansi, kuti tikhale ndi moyo mwa iye.

1 Yohane 4

1 Yohane 4:1-17