1 Yohane 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Okondedwa, musamakhulupirira mzimu uli wonse, koma yesani mizimu ngati icokera mwa Mulungu: popeza aneneri onyenga ambiri anaturuka kulowa m'dziko lapansi.

1 Yohane 4

1 Yohane 4:1-7