1 Yohane 3:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo 6 munthu amene asunga malamulo ace akhala mwa iye, ndi iye mwa munthuyo. Ndipo 7 m'menemo tizindikira kuti akhala mwa ife, kucokera mwa Mzimu amene anatipatsa ife.

1 Yohane 3

1 Yohane 3:21-24