1 Yohane 3:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

osati monga Kaini anali wocokera mwa woipayo, namupha mbale wace. Ndipo anamupha iye cifukwa ninji? Popeza nchiro zace zinali zoipa, ndi za mbaie wace zolungama.

1 Yohane 3

1 Yohane 3:3-17