1 Samueli 9:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anauka mamawa; ndipo kutaca, Samueli anaitana Sauli ali pamwamba pa nyumba, nati, Ukani kuti ndikuloleni mumuke. Ndipo Sauli anauka, naturuka onse awiri, iye ndi Samueli, kunka kunja.

1 Samueli 9

1 Samueli 9:18-27