1 Samueli 31:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nkhondoyo inamkulira Sauli kwambiri, oponya mibvi nampeza; ndipo iye anasautsika kwakukuru cifukwa ca oponya mibviyo.

1 Samueli 31

1 Samueli 31:1-5