1 Samueli 31:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Afilisti anapitikitsa, osawaleka Sauli ndi ana ace; ndipo Afilisti anapha Jonatani, ndi Abinadabu, ndi Malikisua, ana a Sauli.

1 Samueli 31

1 Samueli 31:1-10