1 Samueli 30:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anatsika naye, onani, iwo anabalalika apo ponse, analinkudya, ndi kumwa, ndi kudyerera, cifukwa ca cofunkha zambiri anazitenga ku dziko la Afilisti, ndi ku dziko la Yuda.

1 Samueli 30

1 Samueli 30:6-23