1 Samueli 28:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkaziyo anafika kwa Sauli, naona kuti ali wobvutika kwambiri, nanena naye, Onani, mdzakazi wanu anamvera mau anu, ndipo ndinataya moyo wanga, ndi kumvera mau anu munalankhula ndi ine.

1 Samueli 28

1 Samueli 28:19-23