1 Samueli 26:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Davide ndi Abisai anafika kwa anthuwo usiku; ndipo onani, Sauli anagona tulo m'kati mwa linga la magareta, ndi mkondo wace wozika kumutu kwace; ndi Abineri ndi anthuwo anagona pomzinga iye.

1 Samueli 26

1 Samueli 26:2-15