1 Samueli 26:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Davide anayankha nati kwa Ahimeleki Mhiti, ndi Abisai mwana wa Zeruya, mbale wace wa Yoabu, nati, Adzatsikira nane ndani kumisasako kwa Sauli? Nati Abisai, Nditsika nanu ndine.

1 Samueli 26

1 Samueli 26:1-12