1 Samueli 26:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ici unacicita siciri cabwino. Pali Yehova, muyenera kufa inu, cifukwa simunadikira mbuye wanu, wodzozedwa wa Yehova. Ndipo tsono, penyani mkondo wa mfumu ndi cikho ca madzi zinali kumutu kwace ziri kuti?

1 Samueli 26

1 Samueli 26:7-25