1 Samueli 26:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Davide nati kwa Abineri, Si ndiwe mwamuna weni weni kodi? ndani mwa Aisrayeli afanafana ndi iwe? Unalekeranji tsono kudikira mbuye wako, mfumuyo? pakuti anafika wina kudzaononga mfumu, mbuye wako.

1 Samueli 26

1 Samueli 26:8-24