1 Samueli 25:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakufika anyamata a Davide, analankhula ndi Nabala monga mau aja onse m'dzina la Davide, naleka.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:6-15