1 Samueli 25:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mufunse anyamata anu, adzakuuzani; cifukwa cace muwakomere mtima anyamata awa, pakuti tirikufika tsiku labwino; mupatse ciri conse muli naco m'dzanja lanu, kwa anyamata anu, ndi kwa mwana wanu Davide.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:7-9