1 Samueli 25:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli anamwalira; ndi Aisrayeli onse anaunjikana pamodzi nalira maliro ace, namuika m'nyumba yace ku Rama. Davide nanyamuka, natsikira ku cipululu ca Parana.

1 Samueli 25

1 Samueli 25:1-3