1 Samueli 23:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli ndi anthu ace anamuka kukamfuna. Koma wina anauza Davide; cifukwa cace anatsikira kuthanthweko, nakhala m'cipululu ca Maoni. Ndipo pamene Sauli anamva ici, iye anamlondola Davide m'cipululu ca Maoni.

1 Samueli 23

1 Samueli 23:15-29