1 Samueli 23:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo ananyamuka, namuka ku Zifi asanapiteko Sauli; koma Davide ndi anthu ace anali ku cipululu ca Maoni, m'cigwa ca kumwera kwa cipululu.

1 Samueli 23

1 Samueli 23:15-29