1 Samueli 23:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo awiriwo anapangana pangano pamaso pa Yehova; ndipo Davide anakhala kunkhalango, koma Jonatani anapita ku nyumba yace.

1 Samueli 23

1 Samueli 23:11-24