1 Samueli 23:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono Davide anati, Kodi amuna a ku Keila adzandipereka ine ndi anyamata anga m'dzanja la Sauli? Ndipo Yehova anati, Adzakupereka.

1 Samueli 23

1 Samueli 23:5-22