1 Samueli 23:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi amuna a ku Keila adzandipereka m'dzanja lace? Kodi Sauli adzatsikira ndithu, monga mnyamata wanu wamva? Yehova Mulungu wa Israyeli, ndikupemphani, muuze mnyamata wanu. Ndipo Yehova anati, Adzatsika.

1 Samueli 23

1 Samueli 23:9-15