1 Samueli 20:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anathawa ku Nayoti m'Rama, nadzanena pamaso pa Jonatani, Ndacitanji ine? kuipa kwanga kuli kotani? ndi chimo langa la pamaso pa atate wanu ndi ciani, kuti amafuna moyo wanga?

1 Samueli 20

1 Samueli 20:1-6