1 Samueli 19:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso anabvula zobvala zace, naneneranso pamaso pa Samueli nagona wamarisece usana womwe wonse, ndi usiku womwe wonse. Cifukwa cace amati, Kodi Saulinso ali pakati pa aneneri?

1 Samueli 19

1 Samueli 19:15-24