1 Samueli 19:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mzimu woipa wocokera kwa Yehova unali pa Sauli, pakukhala iye m'nyumba mwace, ndi mkondo wace m'dzanja lace; ndipo Davide anayimba ndi dzanja lace.

1 Samueli 19

1 Samueli 19:1-13