1 Samueli 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anayesa kupyoza Davide kumphatikiza kukhoma ndi mkondowo; koma iye anadzilanditsa kucoka pamaso pa Sauli; ndipo analasa khoma; ndipo Davide anathawa napulumuka usiku uja.

1 Samueli 19

1 Samueli 19:2-11