1 Samueli 19:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco anathawa Davide, napulumuka, nafika kwa Samueli: ku Rama, namuuza zonse Sauli anamcitira. Ndipo iye ndi Samueli anakhala ku Nayoti.

1 Samueli 19

1 Samueli 19:9-24