1 Samueli 19:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Sauli kwa Mikala, Wandinyengeranii comweci, ndi kulola mdani wanga apulumuke? Ndipo Mikala anayankha Sauli, iye anati kwa ine, Undilole ndipite, ndingakuphe.

1 Samueli 19

1 Samueli 19:15-24