1 Samueli 15:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli ananena ndi Sauli, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ace Aisrayeli; cifukwa cace tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova.

1 Samueli 15

1 Samueli 15:1-3