1 Samueli 14:52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali nkhondo yowawa ndi Afilisti masiku onse a Sauli; ndipo Sauli pakuona munthu wamphamvu, kapena ngwazi, anamtenga akhale naye.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:47-52