1 Samueli 14:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi Ahiya mwana wa Ahitubi mbale wace wa Ikabodi, mwana wa Pinehasi, mwana wa Eli, wansembe wa Yehova wa ku Silo, wobvala efodi. Ndipo anthuwo sanadziwa kuti Jonatani wacoka.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:1-10