1 Samueli 14:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali tsiku lina kuti Jonatani mwana wa Sauli ananena ndi mnyamata wonyamula zida zace, Tiye tipite kunka ku kaboma ka Afilisti, tsidya lija. Koma sanauza atate wace.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:1-3