1 Samueli 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwowa anaiwala Yehova Mulungu wao, iye nawapereka m'dzanja la Sisera kazembe wa gulu la Hazori, ndi m'dzanja la Afilisti, ndi m'dzanja la mfumu ya Moabu, iwo naponyana nao.

1 Samueli 12

1 Samueli 12:4-13