1 Samueli 12:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Yakobo anafika ku Aigupto, ndi makolo anu anapemphera kwa Yehova, Yehova anatumiza Mose ndi Aroni, amene anaturutsa makolo anu m'Aigupto, nawakhalitsa pamalo pano,

1 Samueli 12

1 Samueli 12:3-13