1 Samueli 11:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa mithenga inadzayi, Muzitero kwa anthu a ku Yabezi Gileadi, Mawa litatentha dzuwa, mudzaona cipulumutso. Ndipo mithenga inadza niuza a ku Yabezi; nakondwara iwowa.

1 Samueli 11

1 Samueli 11:1-12