1 Samueli 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Samueli anatenga nsupa ya mafuta, nawatsanulira pamutu pace, nampsompsona iye, nati, Sanakudzozani ndi Mulungu kodi, mukhale mfumu ya pa colowa cace?

1 Samueli 10

1 Samueli 10:1-7