1 Petro 5:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wetani gulu la Mulungu liri mwa inu, ndi kuliyang'anira, osati mokangamiza, koma mwaufulu, kwa Mulungu; osatsata phindu lonyansa, koma mwacangu;

1 Petro 5

1 Petro 5:1-7