1 Mbiri 9:40-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

40. Ndipo mwana wa Yonatani ndiye Meribaala; ndi Meribaala anabala Mika.

41. Ndi ana a Mika: Pitoni, ndi Meleki, ndi Tareya, ndi Ahazi.

42. Ndi Ahazi anabala Yara, ndi Yara anabala Ameleti, ndi Azmaveti, ndi Zimri; ndi Zimri anabala Moza,

43. ndi Moza anabala Bineya, ndi Refaya mwana wace, Eleasa mwana wace; Azeli mwana wace;

1 Mbiri 9