1 Mbiri 6:43-54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. mwana wa Yabati, mwana wa Gerisomu, mwana wa Levi.

44. Ndi ku dzanja lamanzere abale ao ana a Merari: Etani mwana wa Kisi, mwana wa Abidi, mwana wa Maluki,

45. mwana wa Hasabiya, mwana wa Amaziya, mwana wa Hilikiya,

46. mwana wa Amzi, mwana wa Bani, mwana wa Semeri,

47. mwana wa Mali, mwana wa Musi, mwana wa Merari, mwana wa Levi.

48. Ndi abale ao Alevi anaikidwa acite za utumiki ziti zonse za kacisi wa nyumba ya Mulungu.

49. Koma Aroni ndi ana ace adafofukiza pa guwa la nsembe yopsereza, ndi pa guwa la nsembe yofukiza, cifukwa ca nchito yonse ya malo opatulikitsa, ndi kucitira Israyeli cowatetezera, monga mwa zonse Mose mtumiki wa Mulungu adawauza.

50. Ndipo ana a Aroni ndiwo Eleazara mwana wace, Pinehasi mwana wace, Abisua mwana wace,

51. Buki mwana wace, Uzi mwana wace, Zerobiya mwana wace,

52. Merayoti mwana wace, Amariya mwana wace, Ahitubu mwana wace,

53. Zadoki mwana wace, Ahimaazi mwana wace.

54. Pokhala pao tsono monga mwa madera ao m'malire mwao ndi awa: kwa ana a Aroni a mabanja a Akobati, pakuti maere oyamba adagwera iwowa,

1 Mbiri 6