1 Mbiri 6:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pokhala pao tsono monga mwa madera ao m'malire mwao ndi awa: kwa ana a Aroni a mabanja a Akobati, pakuti maere oyamba adagwera iwowa,

1 Mbiri 6

1 Mbiri 6:46-57