1 Mbiri 6:26-44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Elikana: ana a Elikana Zofai mwana wace, ndi Nahati mwana wace,

27. Eliabu mwana wace, Yerohamu mwana wace, Elikana mwana wace.

28. Ndi ana a Samueli: woyamba Yoeli, ndi waciwiri Abiya.

29. Ana a Merari: Mali, Libni mwana wace, Simei mwana wace, Uza mwana wace,

30. Simeya mwana wace, Hagiya mwana wace, Asaya mwana wace.

31. Ndipo iwo aja Davide anawaimika a udindo wa nyimbo m'nyumba ya Yehova, litafikira kupumula likasalo, ndi awa.

32. Ndipo anatumikira ndi kuyimba pakhomo pa kacisi wa cihema cokomanako mpaka Solomo adamanga nyumba ya Yehova m'Yerusalemu, naimirira m'utumiki wao monga mwa malongosoledwe ao.

33. Ndipo oimirirawo, ndi ana ao, ndi awa: a ana a Akohati, Hemani woyimbayo, mwana wa Yoeli, mwana wa Samueli,

34. mwana wa Elikana, mwana wa Yerohamu, mwana wa Elieli, mwana wa Towa,

35. mwana wa Zufi, mwana wa Elikana, mwana wa Mahati, mwana wa Amasai,

36. mwana wa Elikana, mwana wa Yoeli, mwana wa Azariya, mwana wa Zefaniya,

37. mwana wa Tahati, mwana wa Asiri, mwana wa Abiasafu, mwana wa Kora,

38. mwana wa Izara, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, mwana wa Israyeli.

39. Ndi mbale wace Asafu wokhala ku dzanja lace lamanja, ndiye Asafu mwana wa Berekiya, mwana wa Simeya,

40. mwana wa Mikaeli, mwana wa Baaseya, mwana wa Malikiya,

41. mwana wa Etini, mwana wa Zera, mwana wa Adaya,

42. mwana wal Edani, mwana wa Zima, mwana wa Simeyi,

43. mwana wa Yabati, mwana wa Gerisomu, mwana wa Levi.

44. Ndi ku dzanja lamanzere abale ao ana a Merari: Etani mwana wa Kisi, mwana wa Abidi, mwana wa Maluki,

1 Mbiri 6