1 Mbiri 6:21-34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Yowa mwana wace, Ido mwana wace, Zera mwana wace, Yeaterai mwana wace.

22. Ana a Kohati: Aminadabu mwana wace, Kora mwana wace, Asiri mwana wace,

23. Elikana mwana wace, ndi Ebiasafu mwana wace, ndi Asiri mwana wace,

24. Tahati mwana wace, Urieli mwana ware, Uziya mwana wace, ndi Sauli mwana wace.

25. Ndi ana a Elikana: Amasai, ndi Ahimoti.

26. Elikana: ana a Elikana Zofai mwana wace, ndi Nahati mwana wace,

27. Eliabu mwana wace, Yerohamu mwana wace, Elikana mwana wace.

28. Ndi ana a Samueli: woyamba Yoeli, ndi waciwiri Abiya.

29. Ana a Merari: Mali, Libni mwana wace, Simei mwana wace, Uza mwana wace,

30. Simeya mwana wace, Hagiya mwana wace, Asaya mwana wace.

31. Ndipo iwo aja Davide anawaimika a udindo wa nyimbo m'nyumba ya Yehova, litafikira kupumula likasalo, ndi awa.

32. Ndipo anatumikira ndi kuyimba pakhomo pa kacisi wa cihema cokomanako mpaka Solomo adamanga nyumba ya Yehova m'Yerusalemu, naimirira m'utumiki wao monga mwa malongosoledwe ao.

33. Ndipo oimirirawo, ndi ana ao, ndi awa: a ana a Akohati, Hemani woyimbayo, mwana wa Yoeli, mwana wa Samueli,

34. mwana wa Elikana, mwana wa Yerohamu, mwana wa Elieli, mwana wa Towa,

1 Mbiri 6