1 Mbiri 4:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo tsono olembedwa maina anadza masiku a Hezekiya mfumu ya Yuda, nakantha mahema ao ndi zokhalamo zao, naziononga konse mpaka lero, nakhala m'malo mwao; popeza panali podyetsa zoweta zao pamenepo.

1 Mbiri 4

1 Mbiri 4:35-43