1 Mbiri 29:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nthawi yoti anakhala mfumu ya Israyeli ndiyo zaka makumi anai; zaka zisanu ndi ziwiri anakhala mfumu m'Hebroni, ndi zaka makumi atatu anakhala mfumu m'Yerusalemu.

1 Mbiri 29

1 Mbiri 29:18-30